Luka 2:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali masiku aja, kuti lamulo linatuluka kwa Kaisara Augusto kuti dziko lonse lokhalamo anthu lilembedwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali masiku aja, kuti lamulo linatuluka kwa Kaisara Augusto kuti dziko lonse lokhalamo anthu lilembedwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Masiku amenewo, Augusto, Mfumu ya ku Roma, adalamula kuti pakhale kalembera wa anthu a m'maiko ake onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mʼmasiku amenewo Kaisara Augusto anapereka lamulo kuti kalembera achitike mʼdziko lonse la Aroma. Onani mutuwo |