Luka 2:5 - Buku Lopatulika5 kukalembedwa iye mwini pamodzi ndi Maria, wopalidwa naye ubwenzi; ndi uyu anali ndi pakati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 kukalembedwa iye mwini pamodzi ndi Maria, wopalidwa naye ubwenzi; ndi uyu anali ndi pakati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Adapita kukalembedwa pamodzi ndi Maria, mkazi wake, amene anali ndi pathupi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iye anapita kumeneko kukalembetsa pamodzi ndi Mariya, amene anapalana naye ubwenzi kuti akwatirane ndipo anali woyembekezera. Onani mutuwo |