Chaka cha mazana asanu ndi limodzi cha moyo wa Nowa, mwezi wachiwiri, tsiku la khumi ndi asanu ndi awiri la mwezi, tsiku lomwelo akasupe onse a madzi aakulu anasefuka, ndi mazenera a kumwamba anatseguka.
Genesis 8:3 - Buku Lopatulika ndipo madzi anaphweraphwerabe padziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo madzi anaphweraphwerabe pa dziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndipo madzi adayamba kutsika pang'onopang'ono. Masiku 150 atapita, madziwo anali atatsika ndithu, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Madzi amaphwabe pa dziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madzi anatsika, |
Chaka cha mazana asanu ndi limodzi cha moyo wa Nowa, mwezi wachiwiri, tsiku la khumi ndi asanu ndi awiri la mwezi, tsiku lomwelo akasupe onse a madzi aakulu anasefuka, ndi mazenera a kumwamba anatseguka.
Ndipo madzi analinkuchepa kufikira mwezi wakhumi; mwezi wakhumi tsiku loyamba mwezi ndipo padaoneka mitu ya mapiri.