Genesis 7:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo anapambana madzi padziko lapansi masiku zana kudza makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo anapambana madzi pa dziko lapansi masiku zana kudza makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Madziwo adakhala osaphwa konse pa dziko lapansi masiku 150. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Madziwo anadzaza dziko lonse lapansi kwa masiku 150. Onani mutuwo |