Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 8:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Madzi amaphwabe pa dziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madzi anatsika,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

3 ndipo madzi anaphweraphwerabe padziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 ndipo madzi anaphweraphwerabe pa dziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 ndipo madzi adayamba kutsika pang'onopang'ono. Masiku 150 atapita, madziwo anali atatsika ndithu,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 8:3
3 Mawu Ofanana  

Pa tsiku la 17 la mwezi wachiwiri, Nowa ali ndi zaka 600, akasupe onse akuya kwambiri anasefuka ndiponso zitseko za madzi akumwamba zinatsekuka.


Madziwo anadzaza dziko lonse lapansi kwa masiku 150.


Madzi anapitirira kuphwa mpaka mwezi wa khumi, ndipo pa tsiku loyamba la mwezi wa khumiwo msonga za mapiri zinayamba kuonekera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa