Genesis 8:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo madzi analinkuchepa kufikira mwezi wakhumi; mwezi wakhumi tsiku loyamba mwezi ndipo padaoneka mitu ya mapiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo madzi analinkuchepa kufikira mwezi wakhumi; mwezi wakhumi tsiku loyamba mwezi ndipo padaoneka mitu ya mapiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Madziwo adanka natsikabe, ndipo pa tsiku loyamba la mwezi wakhumi, nsonga za mapiri zidayamba kuwoneka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Madzi anapitirira kuphwa mpaka mwezi wa khumi, ndipo pa tsiku loyamba la mwezi wa khumiwo msonga za mapiri zinayamba kuonekera. Onani mutuwo |