Genesis 8:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo panali atapita masiku makumi anai, Nowa anatsegula pa zenera la chingalawa limene analipanga: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo panali atapita masiku makumi anai, Nowa anatsegula pa zenera la chingalawa limene analipanga: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Patapita masiku makumi anai, Nowa adatsekula zenera, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Patapita masiku makumi anayi, Nowa anatsekula zenera limene anapanga mʼchombomo Onani mutuwo |