Genesis 8:7 - Buku Lopatulika7 ndipo anatulutsa khwangwala, ndipo anatuluka kunka kwina ndi kwina kufikira adaphwa madzi padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 ndipo anatulutsa khungubwi, ndipo anatuluka kunka kwina ndi kwina kufikira adaphwa madzi pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 natulutsa khwangwala. Khwangwalayo ankangouluka mu mlengalenga kudikira kuti madzi aphwe pa dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 natulutsa khwangwala, koma khwangwalayo ankangowuluka uku ndi uku mpaka madzi anawuma pa dziko lapansi. Onani mutuwo |