Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 8:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo anatulutsa njiwa imchokere, kuti aone kapena madzi anaphwa pamwamba padziko lapansi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo anatulutsa njiwa imchokere, kuti aone kapena madzi anaphwa pamwamba pa dziko lapansi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono Nowa adatulutsa nkhunda kuti ikaone ngati madzi aphwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Kenaka anatulutsa nkhunda kuti aone ngati madzi aphwa pa dziko.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 8:8
7 Mawu Ofanana  

ndipo anatulutsa khwangwala, ndipo anatuluka kunka kwina ndi kwina kufikira adaphwa madzi padziko lapansi.


koma njiwayo siinapeze popondapo phazi lake, nibwera kwa iye kuchingalawako, pakuti madzi analipo padziko lonse lapansi; ndipo anatulutsa dzanja lake, naitenga, nailowetsa kwa iye m'chingalawamo.


Taona, wakongolatu, bwenzi langa; namwaliwe taona, wakongola, maso ako akunga a nkhunda.


Nkhunda yangawe, yokhala m'ming'alu ya thanthwe, mobisika motsetsereka, ndipenye nkhope yako, ndimve mau ako; pakuti mau ako ngokoma, nkhope yako ndi kukongola.


Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa mimbulu; chifukwa chake khalani ochenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa