Genesis 8:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo chingalawa chinaima pamapiri a Ararati, mwezi wachisanu ndi chiwiri, tsiku lakhumi ndi asanu ndi awiri la mwezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo chingalawa chinaima pa mapiri a Ararati, mwezi wachisanu ndi chiwiri, tsiku lakhumi ndi asanu ndi awiri la mwezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 ndipo pa tsiku la 17, mwezi wachisanu ndi chiŵiri, chombocho chidakaima pamwamba pa phiri la Ararati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 ndipo pa tsiku la 17 la mwezi wachisanu ndi chiwiri, chombo chija chinakakhazikika pa mapiri a Ararati. Onani mutuwo |