Genesis 8:3 - Buku Lopatulika3 ndipo madzi anaphweraphwerabe padziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo madzi anaphweraphwerabe pa dziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 ndipo madzi adayamba kutsika pang'onopang'ono. Masiku 150 atapita, madziwo anali atatsika ndithu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Madzi amaphwabe pa dziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madzi anatsika, Onani mutuwo |