Ndipo Yehova anapita atatha kunena naye Abrahamu: ndipo Abrahamu anabwera kumalo kwake.
Genesis 32:1 - Buku Lopatulika Ndipo Yakobo anankabe ulendo wake, ndipo amithenga a Mulungu anakomana naye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yakobo anankabe ulendo wake, ndipo amithenga a Mulungu anakomana naye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yakobe adanyamuka ulendo wake, ndipo angelo a Mulungu adakumana naye. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nayenso Yakobo analowera njira yake, ndipo angelo a Mulungu anakumana naye. |
Ndipo Yehova anapita atatha kunena naye Abrahamu: ndipo Abrahamu anabwera kumalo kwake.
Ndipo anamdalitsa Rebeka, nati kwa iye, Mlongo wathu ndiwe, iwe ukhale amai wa anthu zikwizikwi, mbeu zako zigonjetse chipata cha iwo akudana nao.
Ndipo sunandiloleze ine ndimpsompsone ana anga aamuna ndi aakazi? Wapusa iwe pakuchita chotero.
ngati Paulo, kapena Apolo, kapena Kefa, kapena dziko lapansi, kapena moyo, kapena imfa, kapena za makono ano, kapena zilinkudza; zonse ndi zanu;
kuti mu Mpingo azindikiritse tsopano kwa akulu ndi maulamuliro m'zakumwamba nzeru ya mitundumitundu ya Mulungu,