Aefeso 3:10 - Buku Lopatulika10 kuti mu Mpingo azindikiritse tsopano kwa akulu ndi maulamuliro m'zakumwamba nzeru ya mitundumitundu ya Mulungu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 kuti mu Mpingo azindikiritse tsopano kwa akulu ndi maulamuliro m'zakumwamba nzeru ya mitundumitundu ya Mulungu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsopano afuna kuti kudzera mwa Mpingo, mafumu ndi aulamuliro onse a Kumwamba adziŵe nzeru za Mulungu zamitundumitundu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Cholinga chake tsopano nʼchakuti, kudzera mwa mpingo, mafumu ndi a ulamuliro onse a kumwamba adziwe nzeru zochuluka za Mulungu. Onani mutuwo |