Genesis 32:2 - Buku Lopatulika2 Pamene Yakobo anawaona anati, Ili ndi khamu la Mulungu: ndipo anatcha pamenepo dzina lake Mahanaimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pamene Yakobo anawaona anati, Ili ndi khamu la Mulungu: ndipo anatcha pamenepo dzina lake Mahanaimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ataŵaona, adati, “Ili ndi gulu la ankhondo a Mulungu.” Motero malowo adaŵatcha Mahanaimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pamene Yakobo anawaona anati, “Ili ndi gulu la Mulungu.” Choncho anawatcha malowo Mahanaimu. Onani mutuwo |