Genesis 3:9 - Buku Lopatulika Ndipo Yehova Mulungu anaitana mwamunayo nati kwa iye, Uli kuti? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova Mulungu anaitana mwamunayo nati kwa iye, Uli kuti? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Chauta adamuitana Adamu uja kuti, “Kodi uli kuti?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova Mulungu anayitana munthu uja kuti, “Uli kuti?” |
Ndipo anati, Hagara, mdzakazi wake wa Sarai, ufumira kuti? Unka kuti? Ndipo anati, Ndithawa ine kumaso kwake kwa wakuka wanga Sarai.
Yehova ndipo anati kwa Kaini, Ali kuti Abele mphwako? Ndipo anati, Sindidziwai: kodi ndine woyang'anira mphwanga?
Pamenepo analowa, naima kwa mbuye wake. Ndipo Elisa ananena naye, Ufuma kuti Gehazi? Nati, Ngati mnyamata wanu wayenda konse?