Genesis 18:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anati kwa iye, Ali kuti Sara mkazi wako? Ndipo anati, Taonani m'hemamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anati kwa iye, Ali kuti Sara mkazi wako? Ndipo anati, Taonani m'hemamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono anthuwo adafunsa Abrahamu kuti, “Kodi mkazi wako Sara ali kuti?” Abrahamu adayankha kuti, “Ali m'hemamu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anthuwo anafunsa Abrahamu kuti, “Mkazi wako Sara ali kuti?” Iye anati, “Ali mu tentimu.” Onani mutuwo |