Eksodo 34:8 - Buku Lopatulika Ndipo Mose anafulumira, naweramira pansi nalambira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose anafulumira, naweramira pansi nalambira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo Mose adagwada pansi napembedza. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo Mose anawerama pansi napembedza. |
Ndipo Yehosafati anawerama mutu wake, nkhope yake pansi; ndi Ayuda onse, ndi okhala mu Yerusalemu anagwa pansi pamaso pa Yehova, nalambira Yehova.
Ndipo anthuwo anakhulupirira; ndipo pamene anamva kuti Yehova adawazonda ana a Israele, ndi kuti adaona mazunzo ao, anawerama, nalambira Mulungu.
monga momwe ndinapangana nanu muja munatuluka mu Ejipito, ndi Mzimu wanga unakhala pakati pa inu; musamaopa inu.