Genesis 48:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Yosefe anatulutsa iwo pakati pa maondo ake, nawerama ndi nkhope yake pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Yosefe anatulutsa iwo pakati pa maondo ake, nawerama ndi nkhope yake pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono Yosefe adatenga anawo kuŵachotsa pa maondo a Yakobe. Ndipo adamgwadira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Tsono Yosefe anawachotsa ana aja pa mawondo a Israeli ndipo anamuweramira nkhope pansi. Onani mutuwo |