Eksodo 4:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo anthuwo anakhulupirira; ndipo pamene anamva kuti Yehova adawazonda ana a Israele, ndi kuti adaona mazunzo ao, anawerama, nalambira Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo anthuwo anakhulupirira; ndipo pamene anamva kuti Yehova adawazonda ana a Israele, ndi kuti adaona mazunzo ao, anawerama, nalambira Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Pamenepo Aisraele aja adakhulupiriradi zimenezo. Tsono atamva kuti Chauta adadzaŵayendera ndipo kuti adaona kuzunzika kwaoko, adaŵeramitsa mitu pansi napembedza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 ndipo anakhulupirira. Iwo atamva kuti Yehova anadzawayendera ndi kuti waona mmene akuzunzikira, anaweramitsa mitu pansi napembedza. Onani mutuwo |