Eksodo 4:30 - Buku Lopatulika30 ndipo Aroni anawafotokozera mau onse amene Yehova adauza Mose, nachita zizindikiro zija pamaso pa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 ndipo Aroni anawafotokozera mau onse amene Yehova adauza Mose, nachita zizindikiro zija pamaso pa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Aroni adafotokozera atsogoleriwo zonse zimene Chauta adaauza Mose, ndipo adachita zozizwitsa zonse zija anthuwo akupenya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndipo Aaroni anawafotokozera zonse zimene Yehova ananena kwa Mose. Anachita zizindikirozo pamaso pa anthu onse, Onani mutuwo |