Eksodo 4:29 - Buku Lopatulika29 Pamenepo Mose ndi Aroni anamuka nasonkhanitsa akulu onse a ana a Israele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Pamenepo Mose ndi Aroni anamuka nasonkhanitsa akulu onse a ana a Israele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Motero Mose ndi Aroni adapita, nakasonkhanitsa atsogoleri onse a Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mose ndi Aaroni anapita kukasonkhanitsa pamodzi akuluakulu onse a Aisraeli. Onani mutuwo |