Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 4:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo Mose anauza Aroni mau onse a Yehova amene adamtuma nao, ndi zizindikiro zonse zimene adamlamulira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo Mose anauza Aroni mau onse a Yehova amene adamtuma nao, ndi zizindikiro zonse zimene adamlamulira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Pamenepo Mose adafotokozera Aroni zonse zimene Chauta adaamuuza, pa nthaŵi imene ankamutuma. Adamuuzanso za zozizwitsa zonse zija zimene Chauta adamlamula kuti akachite.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Kenaka Mose anamufotokozera Aaroni chilichonse chimene Yehova anamutuma kuti akanene. Anamufotokozera za zizindikiro zozizwitsa zimene anamulamulira kuti akazichite.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 4:28
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose anadza, naitana akulu a anthu, nawaikira pamaso pao mau awa onse amene Yehova adamuuza.


Ndipo Iye anati, Usayandikire kuno; vula nsapato zako ku mapazi ako, pakuti pamalo pamene upondapo iwe, mpopatulika.


Nyamuka, pita ku Ninive mzinda waukulu uja, nuulalikire uthenga umene ndikuuza.


Ndipo Mose ananena ndi akulu a mafuko a ana a Israele, nati, Chinthu anachilamulira Yehova ndi ichi:


Koma iye anakana, nati, Sindifuna ine; koma pambuyo pake analapa mtima napita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa