Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 4:30 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Ndipo Aaroni anawafotokozera zonse zimene Yehova ananena kwa Mose. Anachita zizindikirozo pamaso pa anthu onse,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

30 ndipo Aroni anawafotokozera mau onse amene Yehova adauza Mose, nachita zizindikiro zija pamaso pa anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 ndipo Aroni anawafotokozera mau onse amene Yehova adauza Mose, nachita zizindikiro zija pamaso pa anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Aroni adafotokozera atsogoleriwo zonse zimene Chauta adaauza Mose, ndipo adachita zozizwitsa zonse zija anthuwo akupenya.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 4:30
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose anabwerera ndi kuyitanitsa akuluakulu. Atabwera anawafotokozera mawu amene Yehova anamulamulira kuti adzanene.


Mose anayankha, “Aisraeliwo sakandikhulupirira ndipo sakandimvera. Iwowo adzati, ‘Yehova sanakuonekere iwe.’ ”


Iwe udzayankhula naye ndi kumuwuza mawu oti akanene. Ine ndidzakuthandizani kuyankhula nonse awirinu ndi kukulangizani zoti mukachite.


Iye akayankhula kwa anthu mʼmalo mwako. Iye adzakhala wokuyankhulira ndipo iweyo udzakhala ngati Mulungu kwa iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa