Ndipo upikule malaya am'kati abafuta a thonje losansitsa, nusoke nduwira wabafuta, nusokenso mpango wopikapika.
Eksodo 29:8 - Buku Lopatulika Ndipo ubwere nao ana ake aamuna ndi kuwaveka malaya am'kati. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ubwere nao ana ake amuna ndi kuwaveka malaya am'kati. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kenaka ubwere ndi ana ake aamuna, ndipo uŵaveke miinjiro. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ubwere ndi ana ake aamuna ndipo uwavekenso minjiro |
Ndipo upikule malaya am'kati abafuta a thonje losansitsa, nusoke nduwira wabafuta, nusokenso mpango wopikapika.
Ndipo usokere ana a Aroni malaya am'kati, nuwasokere mipango; uwasokerenso akapa akhale aulemerero ndi okoma.
Ndipo Mose anatenga ana a Aroni, nawaveka malaya a m'kati, nawamanga m'chuuno ndi mipango, nawamanga akapa; monga Yehova adzauza Mose.