Eksodo 40:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo ubwere nao ana ake aamuna ndi kuwaveka malaya am'kati; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo ubwere nao ana ake amuna ndi kuwaveka malaya am'kati; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ana ake abwerenso, ndipo uŵaveke miinjiro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ubweretse ana ake ndipo uwaveke minjiro. Onani mutuwo |