Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya chihema cha kumbuyo.
Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya Kachisi ya kumbuyo.
Kumbuyo kwake kwa chihemacho, chakuzambwe, upange mafulemu asanu ndi limodzi.
Upange maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo.
Ndipo uzipangira chihema matabwa oimirika, a mtengo wakasiya.
makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.
Nupange matabwa awiri angodya za chihema cha kumbuyo.
Ndi ku mbali ya kumbuyo ya chihema kumadzulo anapanga matabwa asanu ndi limodzi.