Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 36:27 - Buku Lopatulika

27 Ndi ku mbali ya kumbuyo ya chihema kumadzulo anapanga matabwa asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndi ku mbali ya kumbuyo ya Kachisi kumadzulo anapanga matabwa asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Adapanganso mafulemu asanu ndi limodzi kumbuyo kwake kwa chihemacho chakuzambwe,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Anapanganso maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 36:27
4 Mawu Ofanana  

Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya chihema cha kumbuyo.


ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya chihema cha kumbuyo kumadzulo.


makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.


Anapanganso matabwa awiri a kungodya za chihema, m'mbali zake ziwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa