Eksodo 36:28 - Buku Lopatulika28 Anapanganso matabwa awiri a kungodya za chihema, m'mbali zake ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Anapanganso matabwa awiri a kungodya za Kachisi, m'mbali zake ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 ndiponso mafulemu aŵiri am'ngodya, kumbuyo kwake kwa chihemacho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 ndiponso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti. Onani mutuwo |