Eksodo 36:26 - Buku Lopatulika26 makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 ndi masinde ake makumi anai asiliva, masinde aŵiri pansi pa fulemu lililonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 ndiponso matsinde makumi anayi asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse. Onani mutuwo |