Eksodo 36:25 - Buku Lopatulika25 Ndi ku mbali ina ya chihema, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndi ku mbali ina ya Kachisi, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pa mbali yakumpoto ya chihemacho adapanganso mafulemu makumi aŵiri Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Iwo anapanganso maferemu makumi awiri a mbali yakumpoto ya chihemacho, Onani mutuwo |