Eksodo 26:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo uzipangira chihema matabwa oimirika, a mtengo wakasiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo uzipangira Kachisi matabwa oimirika, a mtengo wakasiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 “Upange mafulemu a chihemacho ndi matabwa oimirira bwino a mtengo wa kasiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 “Upange maferemu amatabwa amtengo wa mkesha oyimikira chihemacho. Onani mutuwo |