Eksodo 26:16 - Buku Lopatulika16 Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwali mkono ndi hafu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwali mkono ndi hafu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Muutali mwake fulemu lililonse likhale mamita anai ndi theka, ndipo muufupi mwake masentimita 69. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Feremu iliyonse ikhale yotalika mamita anayi ndipo mulifupi mwake mukhale masentimita 69. Onani mutuwo |