Eksodo 26:17 - Buku Lopatulika17 Pa thabwa limodzi pakhale mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; uzitero pa matabwa onse a chihema. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pa thabwa limodzi pakhale mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; uzitero pa matabwa onse a Kachisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Thabwa lililonse likhale ndi zolumikizira ziŵiri, ndipo mafulemu onse a chihemacho apangidwe ndi matabwa otere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Thabwa lililonse likhale ndi zolumikizira ziwiri. Upange maferemu onse a chihemacho ndi matabwa otere. Onani mutuwo |