Eksodo 26:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo uzipanga matabwa a chihema, matabwa makumi awiri ku mbali ya kumwera, kumwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo uzipanga matabwa a Kachisi, matabwa makumi awiri ku mbali ya kumwera, kumwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Popanga mafulemuwo, ku mbali yakumwera, upange makumi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Upange maferemu makumi awiri a mbali yakummwera kwa chihemacho. Onani mutuwo |