Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Upange maferemu makumi awiri a mbali yakummwera kwa chihemacho.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Ndipo uzipanga matabwa a chihema, matabwa makumi awiri ku mbali ya kumwera, kumwera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo uzipanga matabwa a Kachisi, matabwa makumi awiri ku mbali ya kumwera, kumwera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Popanga mafulemuwo, ku mbali yakumwera, upange makumi aŵiri.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:18
4 Mawu Ofanana  

Kodi maziko ake anawakumba potani, kapena ndani anayika mwala wake wapangodya,


“Upange maferemu amatabwa amtengo wa mkesha oyimikira chihemacho.


Thabwa lililonse likhale ndi zolumikizira ziwiri. Upange maferemu onse a chihemacho ndi matabwa otere.


Ndipo upange matsinde 40 asiliva ndipo uwayike pansi pa maferemuwo. Pansi pa feremu iliyonse pakhale matsinde awiri ogwiriziza zolumikizira ziwiri zija.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa