Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:22 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Upange maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

22 Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya chihema cha kumbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya Kachisi ya kumbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Kumbuyo kwake kwa chihemacho, chakuzambwe, upange mafulemu asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:22
4 Mawu Ofanana  

“Upange maferemu amatabwa amtengo wa mkesha oyimikira chihemacho.


Upangenso matsinde 40 asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse.


Ndipo upangenso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti.


Anapanganso maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa