Eksodo 26:23 - Buku Lopatulika23 Nupange matabwa awiri angodya za chihema cha kumbuyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Nupange matabwa awiri angodya za Kachisi za kumbuyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Kumbuyo kwa chihema konko, pangodya pakhale mafulemu aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndipo upangenso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti. Onani mutuwo |