Eksodo 26:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya chihema cha kumbuyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo uzipanga matabwa asanu ndi limodzi kwa mbali ya Kachisi ya kumbuyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Kumbuyo kwake kwa chihemacho, chakuzambwe, upange mafulemu asanu ndi limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Upange maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo. Onani mutuwo |