Eksodo 26:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo akhale ophatikizika pamodzi patsinde, nakhalenso ophatikizika pamodzi kumutu kwake ndi mphete imodzi; azitero onse awiri; azikhala angodya ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo akhale ophatikizika pamodzi patsinde, nakhalenso ophatikizika pamodzi kumutu kwake ndi mphete imodzi; azitero onse awiri; azikhala angodya ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Mafulemu ameneŵa apangodya azilumikizidwa kuyambira pansi mpaka pa chigwinjiri chapamwamba. Umu ndimo m'mene akhalire mafulemu aŵiri amene akupanga ngodya ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pa ngodya ziwirizi pakhale maferemu awiri, kuyambira pansi mpaka pamwamba ndipo alumikizidwe pa ngowe imodzi. Maferemu onse akhale ofanana. Onani mutuwo |