Eksodo 26:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo pakhale matabwa asanu ndi atatu, ndi makamwa ao asiliva, ndiwo makamwa khumi mphambu asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo pakhale matabwa asanu ndi atatu, ndi makamwa ao asiliva, ndiwo makamwa khumi mphambu asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Motero padzakhala mafulemu asanu ndi atatu okhala ndi masinde ake 16 asiliva, aŵiri pansi pa fulemu lililonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Choncho pakhale maferemu asanu ndi atatu ndiponso matsinde 16 asiliva, awiri akhale pansi pa feremu iliyonse. Onani mutuwo |