Eksodo 26:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo uzipanga mitanda ya mtengo wakasiya; isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo uzipanga mitanda ya mtengo wakasiya; isanu ya matabwa a pa mbali ina ya Kachisi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 “Upange mitanda ya mtengo wa kasiya, isanu pa mafulemu a mbali ina ya chihema, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Upange mitanda ya matabwa amtengo wa mkesha: mitanda isanu ikhale ya maferemu a mbali imodzi ya chihema, Onani mutuwo |