Eksodo 26:27 - Buku Lopatulika27 ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya chihema cha kumbuyo kumadzulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya Kachisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya Kachisi ya kumbuyo kumadzulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 ndi isanu inanso pa mafulemu a mbali ina. Pakhalenso mitanda isanu pa mafulemu akuzambwe chakumbuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 mitanda isanu inanso ikhale ya maferemu a mbali inayo. Pakhalenso mitanda ina isanu ya mbali yakumadzulo, kumapeto kwenikweni kwa chihema. Onani mutuwo |