Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 26:28 - Buku Lopatulika

28 Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Mtanda wa pakati penipeni pa mafulemuwo ugwire mafulemu onse, kuyambira ku mapeto mpaka ku mapeto.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Mtanda wapakati pa maferemuwo uchokere pa maferemu a mbali ina mpaka mbali inanso.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:28
3 Mawu Ofanana  

ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya chihema cha kumbuyo kumadzulo.


Ndipo uzikuta matabwa ndi golide, ndi kupanga mphete zao zagolide zopisamo mitandayo; uzikutanso mitandayo ndi golide.


Ndipo anapititsa mtanda wa pakatipo, pakati pa matabwa kufikira kuthungo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa