Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 26:29 - Buku Lopatulika

29 Ndipo uzikuta matabwa ndi golide, ndi kupanga mphete zao zagolide zopisamo mitandayo; uzikutanso mitandayo ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ndipo uzikuta matabwa ndi golide, ndi kupanga mphete zao zagolide zopisamo mitandayo; uzikutanso mitandayo ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Mafulemuwo uŵakute ndi golide, ndi kulonganso mphete zagolide m'mafulemuwo kuti agwirizire mitanda ija, ndipo mitandayo ikhale yokutidwa ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Maferemuwo uwakute ndi golide ndiponso upange mphete zagolide zogwiriziza mitandayo. Ndipo mitandayonso uyikute ndi golide.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:29
6 Mawu Ofanana  

Ndipo m'kati mwa chipindacho, m'litali mwake munali mikono makumi awiri, kupingasa kwake mikono makumi awiri, ndi msinkhu wake mikono makumi awiri, kupingasa kwake mikono makumi awiri, ndi msinkhu wake mikono makumi awiri; ndipo anamukuta ndi golide wayengetsa, nakutanso guwa la nsembe ndi matabwa amkungudza.


Ndipo nyumba yonse anaikuta ndi golide mpaka adatha nyumba yonse, ndi guwa lonse la nsembe linali chakuno cha chipinda chamkati analikuta ndi golide.


Mphetezo zikhale pafupi pa mitanda, zikhale zopisamo mphiko za kunyamulira nazo gome.


Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo.


Ndipo uutse chihema monga mwa makhalidwe ake amene anakusonyeza m'phiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa