Eksodo 26:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo uutse chihema monga mwa makhalidwe ake amene anakusonyeza m'phiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo uutse Kachisi monga mwa makhalidwe ake amene anakusonyeza m'phiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Motero upange chihema changa monga momwe ndikukulangizira paphiri pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 “Upange chihema mofanana ndi momwe ndinakuonetsera pa phiri paja. Onani mutuwo |