Eksodo 26:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo uziomba nsalu yotchinga ya thonje lamadzi, ndi lofiirira ndi lofiira, ndi la bafuta wa thonje losansitsa, aiombe ndi akerubi ntchito ya mmisiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo uziomba nsalu yotchinga ya thonje lamadzi, ndi lofiirira ndi lofiira, ndi la bafuta wa thonje losansitsa, aiombe ndi akerubi ntchito ya mmisiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Usoke nsalu yotchingira yobiriŵira, yofiirira ndi yofiira, ndiponso ya bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino. Ndipo nsaluyo uipete ndi zithunzi za akerubi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Upange nsalu yokhala ndi mtundu wamtambo, wapepo ndi ofiira ndipo nsaluyo ikhale yolukidwa bwino, yofewa ndi yosalala. Ndipo anthu aluso apetepo zithunzi za Akerubi. Onani mutuwo |