Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:30 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 “Upange chihema mofanana ndi momwe ndinakuonetsera pa phiri paja.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

30 Ndipo uutse chihema monga mwa makhalidwe ake amene anakusonyeza m'phiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ndipo uutse Kachisi monga mwa makhalidwe ake amene anakusonyeza m'phiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Motero upange chihema changa monga momwe ndikukulangizira paphiri pano.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:30
14 Mawu Ofanana  

Davide anati, “Zonsezi ndalemba kuchokera kwa Yehova, ndipo Iye wachita kuti ndimvetsetse zonse za mapulaniwa.”


Uwonetsetse kuti wapanga zonse monga momwe ndikukuonetsera pa phiri pano.”


Umange chihema ndiponso ziwiya zamʼkatimo monga momwe Ine ndidzakuonetsere.


Maferemuwo uwakute ndi golide ndiponso upange mphete zagolide zogwiriziza mitandayo. Ndipo mitandayonso uyikute ndi golide.


Guwalo likhale lamatabwa ndi logoba mʼkati mwake. Ulipange monga momwe ndinakuonetsera pa phiri paja.


“Imika chihema, tenti ya msonkhano, tsiku loyamba la mwezi.


Kenaka Akohati ananyamuka atanyamula zinthu zopatulika. Chihema chinkayenera kuyimikidwa iwo asanafike.


Choyikapo nyalecho chinapangidwa motere: chinasulidwa kuchokera ku golide, kuyambira pa tsinde pake mpaka ku maluwa ake. Choyikapo nyalecho chinapangidwa monga momwe Yehova anaonetsera Mose.


“Makolo athu anali ndi tenti ya msonkhano pakati pawo mʼchipululu. Anayipanga monga momwe Mulungu anawuzira Mose, molingana ndi chithunzi chimene Mose anachiona.


Ndipo akutumikira mʼmalo opatulika, mu Tenti yeniyeni yoyikidwa ndi Ambuye, osati ndi munthu.


Iwo amatumikira pamalo opatulika amene ndi chithunzi ndi chifanizo cha zimene zili kumwamba. Ichi ndi chifukwa chake Mose anachenjezedwa pamene anali pafupi kumanga Tenti: “Uwonetsetse kuti wapanga zonse monga momwe ndikukuonetsera pa phiri pano.”


Tsono panafunika kuti zinthu zingofanizira zenizeni za kumwamba, ziyeretsedwe ndi nsembe zimenezi, koma zinthu za kumwamba zenizenizo kuti ziyeretsedwe panafunika nsembe zina zoposa zimenezo.


Atagonjetsa dziko lonse Aisraeli anasonkhana ku Silo ndipo anayimikako tenti ya msonkhano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa