Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:23 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ndipo upangenso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

23 Nupange matabwa awiri angodya za chihema cha kumbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Nupange matabwa awiri angodya za Kachisi za kumbuyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Kumbuyo kwa chihema konko, pangodya pakhale mafulemu aŵiri.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:23
3 Mawu Ofanana  

Kumbuyo kwa Nyumbayo anadula chipinda chachitali mamita asanu ndi anayi. Chipindachi anachimanga ndi matabwa a mkungudza kuyambira pansi mpaka ku denga kuti chikhale chipinda chopatulika chamʼkati mwa Nyumba ya Mulungu ngati Malo Wopatulika Kwambiri.


Upange maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo.


Pa ngodya ziwirizi pakhale maferemu awiri, kuyambira pansi mpaka pamwamba ndipo alumikizidwe pa ngowe imodzi. Maferemu onse akhale ofanana.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa