Pamene anapitirira pa Amfipoli, ndi Apoloniya, anafika ku Tesalonika, kumene kunali sunagoge wa Ayuda.
Afilipi 4:16 - Buku Lopatulika pakuti mu Tesalonikanso munanditumizira pa chosowa changa kamodzi kapena kawiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 pakuti m'Tesalonikanso munanditumizira pa chosowa changa kamodzi kapena kawiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene ndinali ku Tesalonika, mudatumiza kangapo zondithandiza pa zosoŵa zanga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pakuti ngakhale pamene ndinali ku Tesalonika, munanditumizira kangapo zondithandiza pa zosowa zanga. |
Pamene anapitirira pa Amfipoli, ndi Apoloniya, anafika ku Tesalonika, kumene kunali sunagoge wa Ayuda.
chifukwa tinafuna kudza kwa inu, inedi Paulo ndatero kamodzi kapena kawiri; koma Satana anatiletsa.
Pakuti mukumbukira, abale, chigwiritso chathu ndi chivuto chathu; pochita usiku ndi usana, kuti tingalemetse wina wa inu, tinalalikira kwa inu Uthenga Wabwino wa Mulungu.
Ndipo anthu athu aphunzirenso asunge ntchito zabwino zofunika, kuti asakhale osabala zipatso.