Ndipo tsopano, mbuye wanga mfumu, maso a Aisraele onse ali pa inu, kuti muwauze amene adzakhala pa mpando wachifumu wa mbuye wanga mfumu atamuka iye.
2 Samueli 23:2 - Buku Lopatulika Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Mzimu wa Chauta ukulankhula mwa ine, mau ake ali pakamwa panga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Mzimu wa Yehova unayankhula kudzera mwa ine; mawu ake anali pakamwa panga. |
Ndipo tsopano, mbuye wanga mfumu, maso a Aisraele onse ali pa inu, kuti muwauze amene adzakhala pa mpando wachifumu wa mbuye wanga mfumu atamuka iye.
Davide mwini yekha anati mwa Mzimu Woyera, Ambuye anati kwa Ambuye wanga, Khala kudzanja langa lamanja, kufikira ndiwaika adani ako popondapo mapazi ako.
pakuti kale lonse chinenero sichinadze ndi chifuniro cha munthu; koma anthu a Mulungu, ogwidwa ndi Mzimu Woyera, analankhula.